Salimo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+ Salimo 77:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama. Miyambo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+ Miyambo 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+ Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+
6 Usiku ndidzakumbukira nyimbo zanga zoimbidwa ndi chipangizo cha zingwe.+Ndidzasonyeza kudera nkhawa mumtima mwanga,+Ndipo ndidzasinkhasinkha zinthu zonse mozama.
28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+