Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+

  • 2 Mbiri 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.

  • Mlaliki 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Komanso, munthu aliyense amene Mulungu woona wam’patsa chuma ndiponso zinthu zambiri,+ ndiye kuti wamulola kuti adye kuchokera pa zinthuzo.+ Wamulolanso kuti alandire mphoto yake ndi kusangalala chifukwa cha ntchito yake imene amaigwira mwakhama.+ Imeneyi ndi mphatso yochokera kwa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena