8 Kukoma mtima kwakukulu kumeneku kunapatsidwa kwa ine, munthu wochepa pondiyerekeza ndi wochepetsetsa+ wa oyera onse. Ndinapatsidwa kukoma mtima kumeneku+ kuti ndilengeze kwa mitundu ina+ uthenga wabwino wonena za chuma chopanda polekezera+ cha Khristu,