1 Mafumu 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+ 1 Mafumu 4:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+ 1 Mafumu 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+ Akolose 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chuma chonse chokhudzana ndi nzeru ndiponso kudziwa zinthu+ chinabisidwa mosamala mwa iye.
12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+
29 Mulungu anapitiriza kupatsa Solomo nzeru zopanda malire ndi luso lomvetsa zinthu losaneneka.+ Anam’patsanso mtima wozindikira zinthu mwakuya.+
34 Ndipo anthu ankabwera kuchokera ku mitundu yonse kudzamva nzeru za Solomo,+ ngakhalenso kuchokera kwa mafumu onse a padziko lapansi amene anamva za nzeru zake.+