Deuteronomo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+ Mlaliki 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kwa munthu, palibe chabwino kuposa kuti adye, amwe, ndi kusangalatsa mtima wake chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ineyo ndaona kuti zimenezinso n’zochokera m’dzanja la Mulungu woona.+
10 “Mukadzadya ndi kukhuta+ mudzatamandenso+ Yehova Mulungu wanu, chifukwa cha dziko labwino limene wakupatsani.+
24 Kwa munthu, palibe chabwino kuposa kuti adye, amwe, ndi kusangalatsa mtima wake chifukwa choti wagwira ntchito mwakhama.+ Ineyo ndaona kuti zimenezinso n’zochokera m’dzanja la Mulungu woona.+