1 Mbiri 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Yehova anapitiriza kukweza Solomo+ pamaso pa Aisiraeli onse, ndi kum’patsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+ 2 Mbiri 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi. Mlaliki 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso ndinali kuchitabe zinthu mwanzeru.+
25 Yehova anapitiriza kukweza Solomo+ pamaso pa Aisiraeli onse, ndi kum’patsa ulemu waukulu wachifumu kuposa mfumu ina iliyonse imene inalamulira Isiraeli iye asanakhale mfumu.+
22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
9 Ndinali ndi zinthu zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso ndinali kuchitabe zinthu mwanzeru.+