1 Mafumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+ 1 Mafumu 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.
13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+
23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.