Yobu 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikapitiriza kudikira, ku Manda kukhala kunyumba kwanga.+Ndidzayala bedi langa mu mdima.+ Yobu 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti ndikudziwa bwino kuti mudzandibwezera ku imfa,+Kunyumba yosonkhanako aliyense wamoyo. Salimo 49:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+ Mlaliki 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+
14 Awatsogolera ku Manda ngati nkhosa zopita kokaphedwa.+Imfa idzakhala m’busa wawo.+Ndipo m’mawa anthu owongoka mtima adzawalamulira.+Matupi awo adzawonongeka.+Aliyense wa iwo malo ake okhala ndi ku Manda, osati malo okwezeka.+
10 Chilichonse chimene dzanja lako lapeza kuti lichite, uchichite ndi mphamvu zako zonse,+ pakuti kulibe kugwira ntchito, kuganiza zochita, kudziwa zinthu,+ kapena nzeru,+ ku Manda*+ kumene ukupitako.+