Yobu 15:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aimvi ndi okalamba ali pakati pathu,+Omwe ali akale kuposa bambo ako. Miyambo 16:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Imvi ndizo chisoti chachifumu cha ulemerero+ zikapezeka m’njira yachilungamo.+