Yobu 32:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa.
6 Kenako Elihu mwana wa Barakeli mbadwa ya Buza anati:“Ine ndine wamng’onoNdipo amuna inu ndinu achikulire.+N’chifukwa chake ndinabweza mawu anga ndipo ndinaopaKukuuzani zimene ndikudziwa.