1 Mafumu 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.” 2 Mbiri 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pomalizira pake Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+
21 Zomwe zidzachitike n’zoti, inuyo mbuyanga mfumu mukadzangogona m’manda limodzi ndi makolo anu,+ ineyo ndi mwana wanga Solomo tidzaoneka ngati olakwa.”
31 Pomalizira pake Solomo anagona pamodzi ndi makolo ake, ndipo anaikidwa m’manda mu Mzinda wa Davide bambo ake.+ Kenako mwana wake Rehobowamu,+ anayamba kulamulira m’malo mwake.+