1 Mbiri 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+ 2 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo. Mlaliki 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo kodi ndani angadziwe kuti kaya adzakhala wanzeru kapena wopusa?+ Koma adzatenga zinthu zanga zonse zimene ndinazipeza movutikira ndiponso zimene ndinazichita mwanzeru padziko lapansi pano.+ Zimenezinso n’zachabechabe. Mateyu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Solomo anabereka Rehobowamu.+Rehobowamu anabereka Abiya.Abiya+ anabereka Asa.+
10 Mwana wa Solomo anali Rehobowamu.+ Rehobowamu anabereka Abiya,+ Abiya anabereka Asa,+ Asa anabereka Yehosafati,+
7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo.
19 Ndipo kodi ndani angadziwe kuti kaya adzakhala wanzeru kapena wopusa?+ Koma adzatenga zinthu zanga zonse zimene ndinazipeza movutikira ndiponso zimene ndinazichita mwanzeru padziko lapansi pano.+ Zimenezinso n’zachabechabe.