2 Mbiri 20:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Yehosafati+ anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba+ mwana wa Sili.
31 Yehosafati+ anapitiriza kulamulira ku Yuda. Iye anali ndi zaka 35 pamene anayamba kulamulira ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 25. Mayi ake dzina lawo linali Azuba+ mwana wa Sili.