1 Mafumu 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye sanamvere malangizo ochokera kwa akulu aja, m’malomwake anayamba kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi,+ omwe anali kumutumikira.+ 2 Mbiri 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali.+ Chotero Mfumu Rehobowamu inasiya malangizo+ a akulu aja.+ 2 Mbiri 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+
8 Koma iye sanamvere malangizo ochokera kwa akulu aja, m’malomwake anayamba kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi,+ omwe anali kumutumikira.+
13 Mfumuyo inayamba kuyankha anthuwo mwaukali.+ Chotero Mfumu Rehobowamu inasiya malangizo+ a akulu aja.+
9 Chotero Sisaki+ mfumu ya Iguputo anaukira Yerusalemu ndi kutenga chuma cha m’nyumba ya Yehova+ ndi chuma cha m’nyumba ya mfumu.+ Anatenga chilichonse kuphatikizapo zishango zagolide zimene Solomo anapanga.+