Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Davide anauza Yonatani kuti: “Nanga adzandiuza ndani ngati bambo ako akuyankha mwaukali?”

  • Miyambo 10:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakamwa pa wolungama m’pamene pamachokera moyo,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamabisa zachiwawa.+

  • Miyambo 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munthu woipa amakodwa ndi kuchimwa kwa milomo yake,+ koma wolungama amachoka m’masautso.+

  • Miyambo 14:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Munthu wanzeru amachita mantha ndipo amapatuka pa choipa,+ koma wopusa amapsa mtima ndiponso amakhala wodzidalira.+

  • Miyambo 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyankha modekha kumabweza mkwiyo,+ koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+

  • Aefeso 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Kuwawidwa mtima konse kwa njiru,+ kupsa mtima, mkwiyo, kulalata ndiponso mawu achipongwe+ zichotsedwe mwa inu limodzi ndi zoipa zonse.+

  • Aefeso 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Inu ambuye, muzichitiranso akapolo anu chimodzimodzi ndipo muleke kuwaopseza,+ pakuti mukudziwa kuti Ambuye wa nonsenu, wa iwowo ndi wa inuyo,+ ali kumwamba ndipo alibe tsankho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena