Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+ Miyambo 24:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kwa munthu wopusa, nzeru zenizeni n’chinthu chapatali.+ Iye satsegula pakamwa pake pachipata cha mzinda. Yesaya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzaika anyamata kuti akhale akalonga awo ndipo anthu ankhanza adzawalamulira.+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
7 Kwa munthu wopusa, nzeru zenizeni n’chinthu chapatali.+ Iye satsegula pakamwa pake pachipata cha mzinda.