Miyambo 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Munthu wonyoza amafunafuna nzeru ndipo sazipeza. Koma kudziwa zinthu kumakhala kosavuta kwa munthu womvetsa zinthu.+ 1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
6 Munthu wonyoza amafunafuna nzeru ndipo sazipeza. Koma kudziwa zinthu kumakhala kosavuta kwa munthu womvetsa zinthu.+
14 Koma munthu wokonda zinthu za m’dziko* salandira zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa,+ chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.