Oweruza 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+ Mlaliki 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa?
25 Masiku amenewo mu Isiraeli munalibe mfumu.+ Aliyense anali kuchita zimene anali kuona kuti n’zoyenera.+
16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa?