2 Mbiri 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo. 2 Mbiri 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu+ ndi masiku 10 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+ Yesaya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzaika anyamata kuti akhale akalonga awo ndipo anthu ankhanza adzawalamulira.+
7 Ndipo anthu osowa chochita+ ndi opanda pake+ anasonkhana kumbali yake. Pamapeto pake iwo anakhala amphamvu kuposa Rehobowamu+ mwana wa Solomo pamene Rehobowamuyo anali wamng’ono komanso wamantha,+ ndipo sanathe kulimbana nawo.
9 Yehoyakini+ anali ndi zaka 18 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira miyezi itatu+ ndi masiku 10 ku Yerusalemu. Iye anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova.+