Yeremiya 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+ Mateyu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.+Salatiyeli anabereka Zerubabele.+
24 “‘Pali ine, Mulungu wamoyo,’ watero Yehova, ‘ngakhale iwe Koniya+ mwana wa Yehoyakimu,+ mfumu ya Yuda, utakhala mphete yodindira+ kudzanja langa lamanja, ndidzakuvula!+
12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.+Salatiyeli anabereka Zerubabele.+