Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ana a Pedaya anali Zerubabele+ ndi Simeyi. Ana a Zerubabele anali Mesulamu ndi Hananiya, (Selomiti anali mlongo wawo),

  • Ezara 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ndi abale ake ansembe, ndiponso Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi abale ake, ananyamuka n’kumanga guwa lansembe la Mulungu wa Isiraeli kuti aziperekerapo nsembe zopsereza, mogwirizana ndi zimene zinalembedwa+ m’chilamulo cha Mose munthu wa Mulungu woona.

  • Nehemiya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Otsatirawa anali ansembe ndi Alevi amene anapita ndi Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa:+ Seraya, Yeremiya, Ezara,

  • Luka 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 mwana wa Yoanani,

      mwana wa Resa,

      mwana wa Zerubabele,+

      mwana wa Salatiyeli,+

      mwana wa Neri,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena