Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koresi mfumu ya Perisiya anatuma msungichuma Mitiredati yemwe anabweretsa ziwiyazo n’kuziwerenga. Atatero anazipereka kwa Sezibazara*+ mtsogoleri wa Yuda.+

  • Ezara 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Panali pa nthawi imeneyi pamene Zerubabele+ mwana wa Salatiyeli+ ndi Yesuwa+ mwana wa Yehozadaki ananyamuka n’kuyamba kumanganso nyumba ya Mulungu. Nyumbayi inali ku Yerusalemu ndipo panali aneneri a Mulungu+ omwe anali kuwathandiza.

  • Hagai 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Chonde, kauze Zerubabele,+ mwana wa Salatiyeli+ bwanamkubwa wa Yuda,+ Yoswa+ mwana wa Yehozadaki+ mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse kuti,

  • Hagai 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “‘Koma tsopano limba mtima iwe Zerubabele. Limba mtima+ iwe Yoswa mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe,’ watero Yehova.

      “‘Limbani mtima anthu nonse a m’dzikoli ndipo gwirani ntchito,’+ watero Yehova.

      “‘Pakuti ine ndili ndi inu,’+ watero Yehova wa makamu.

  • Zekariya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Choncho iye anandiuza kuti: “Yehova wauza Zerubabele kuti, ‘“Kuti zinthu zonsezi zichitike, sipakufunika gulu lankhondo,+ kapena mphamvu,+ koma mzimu wanga,”+ watero Yehova wa makamu.

  • Mateyu 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ayuda atatengedwa kupita ku Babulo, Yekoniya anabereka Salatiyeli.+

      Salatiyeli anabereka Zerubabele.+

  • Luka 3:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 mwana wa Yoanani,

      mwana wa Resa,

      mwana wa Zerubabele,+

      mwana wa Salatiyeli,+

      mwana wa Neri,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena