Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 22:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Zinthu zidzakuyendera bwino+ ukayesetsa kutsatira malamulo+ ndi zigamulo+ zimene Yehova analamula+ Mose zokhudza Isiraeli. Khala wolimba mtima ndipo uchite zinthu mwamphamvu.+ Usaope+ kapena kuchita mantha.+

  • Zekariya 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Limbani mtima anthu inu ndipo mukonzeke kugwira ntchito,+ inu amene mukumva mawu a aneneri masiku ano.+ Awa ndi mawu amene aneneriwo ananena pa tsiku limene maziko a nyumba ya Yehova wa makamu anayalidwa kuti kachisi amangidwe.+

  • 1 Akorinto 16:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Khalani maso,+ limbani m’chikhulupiriro,+ pitirizani kuchita chamuna,+ khalani amphamvu.+

  • Aefeso 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Potsiriza ndikuti, pitirizani kupeza mphamvu+ kuchokera kwa Ambuye ndiponso kuchokera ku mphamvu+ zake zazikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena