Yeremiya 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ponena za nyumba ya mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti, ‘Kwa ine, iwe uli ngati Giliyadi ndiponso ngati nsonga ya phiri la ku Lebanoni.+ Ndithudi ndidzakusandutsa chipululu+ ndipo m’mizinda iyi simudzapezeka aliyense wokhalamo.+
6 “Ponena za nyumba ya mfumu ya Yuda, Yehova wanena kuti, ‘Kwa ine, iwe uli ngati Giliyadi ndiponso ngati nsonga ya phiri la ku Lebanoni.+ Ndithudi ndidzakusandutsa chipululu+ ndipo m’mizinda iyi simudzapezeka aliyense wokhalamo.+