Salimo 107:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Nthaka yobala zipatso amaisandutsa dziko lamchere,+Chifukwa cha kuipa kwa anthu okhala mmenemo. Yesaya 27:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri udzatsala wokhawokha. Malo odyetserako ziweto adzakhala opanda kanthu ndipo adzasiyidwa ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ng’ombe azidzadya msipu ndipo azidzagona pansi. Iye adzadya nthambi zake.+
10 Pakuti mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri udzatsala wokhawokha. Malo odyetserako ziweto adzakhala opanda kanthu ndipo adzasiyidwa ngati chipululu.+ Kumeneko mwana wa ng’ombe azidzadya msipu ndipo azidzagona pansi. Iye adzadya nthambi zake.+