-
2 Mbiri 10:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Popeza kuti mfumuyo sinawamvere Aisiraeli onsewo, iwo anayankha mfumuyo kuti: “Tili ndi gawo lanji mwa Davide?+ Ife tilibe cholowa mwa mwana wa Jese.+ Aisiraeli inu, aliyense apite kwa milungu yake!+ Tsopano iwe Davide,+ uzisamalira nyumba yako yokha.” Aisiraeliwo atatero, onse anayamba kubwerera kumahema awo.
-