2 Mbiri 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye sanamvere malangizo+ ochokera kwa akulu aja, m’malomwake anayamba kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi,+ omwe anali kum’tumikira.+
8 Koma iye sanamvere malangizo+ ochokera kwa akulu aja, m’malomwake anayamba kukafunsira malangizo kwa achinyamata amene anakulira naye limodzi,+ omwe anali kum’tumikira.+