Miyambo 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mwana wanga ukasiya kumvera malangizo, ndiye kuti wapatuka pa mawu okudziwitsa zinthu.+