Miyambo 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Upeze nzeru,+ upezenso luso lomvetsa zinthu.+ Usaiwale ndipo usapatuke pa mawu a m’kamwa mwanga.+ Miyambo 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Wodzipatula amafunafuna zolakalaka zake zosonyeza kudzikonda.+ Iye amachita zosemphana ndi nzeru zonse zopindulitsa.+ Luka 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+
18 Wodzipatula amafunafuna zolakalaka zake zosonyeza kudzikonda.+ Iye amachita zosemphana ndi nzeru zonse zopindulitsa.+
18 Choncho muzimvetsera mwatcheru kwambiri. Pakuti amene ali nazo, adzapatsidwa zochuluka,+ koma amene alibe, adzalandidwa ngakhalenso zimene akuganizira kuti ali nazo.”+