2 Mbiri 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira za Davide kholo lake.+ Sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+ Salimo 44:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zonsezi ndi zimene zatigwera, koma sitinakuiwaleni,+Sitinachite mwachinyengo ndi pangano lanu.+ Miyambo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwana wanga, usaiwale lamulo langa,+ ndipo mtima wako usunge malamulo anga.+
2 Iye anachita zoyenera pamaso pa Yehova+ ndipo anayenda m’njira za Davide kholo lake.+ Sanapatukire mbali ya kudzanja lamanja kapena lamanzere.+