Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iwo alola ena mwa ana aakazi a mitundu inayo kuti akhale akazi awo ndi akazi a ana awo aamuna,+ ndipo iwo omwe ndi mtundu wopatulika,+ asakanikirana+ ndi anthu a mitundu ina. Akalonga ndi atsogoleri ndiwo ali patsogolo+ pa kusakhulupirika kumeneku.”

  • Ezara 9:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 kodi zoona tiphwanyenso malamulo anu kachiwiri ndi kupanga mapangano a ukwati+ ndi anthu a mitundu ina ochita zonyansawa?+ Kodi tikatero simutikwiyira koopsa+ mwakuti sipakhalanso wotsala+ ndi wopulumuka?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena