Deuteronomo 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikananena kuti: “Ndidzawabalalitsa,+Ndidzachititsa anthu kuti asatchule n’komwe za iwo,”+ Yesaya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+ Ezekieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “‘“Zimenezi zikadzachitika, ndidzachititsa kuti ena a inu asaphedwe ndi lupanga pakati pa mitundu ya anthu, mukadzamwazikana kupita kumayiko osiyanasiyana.+
9 Yehova wa makamu akanapanda kutisiyira anthu ochepa opulumuka,+ tikanakhala ngati Sodomu, ndipo tikanafanana ndi Gomora.+
8 “‘“Zimenezi zikadzachitika, ndidzachititsa kuti ena a inu asaphedwe ndi lupanga pakati pa mitundu ya anthu, mukadzamwazikana kupita kumayiko osiyanasiyana.+