Ezekieli 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ndidzachititsa kuti pakhale anthu ena opulumuka, chifukwa ena a inu simudzaphedwa ndi lupanga pakati pa anthu a mitundu ina mukadzabalalikira mʼmayiko osiyanasiyana.+
8 Koma ndidzachititsa kuti pakhale anthu ena opulumuka, chifukwa ena a inu simudzaphedwa ndi lupanga pakati pa anthu a mitundu ina mukadzabalalikira mʼmayiko osiyanasiyana.+