Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma iwe Yakobo mtumiki wanga usachite mantha,” akutero Yehova,

      “Ndipo iwe Isiraeli usaope.+

      Chifukwa ndidzakupulumutsa kuchokera kutali

      Ndidzapulumutsanso ana ako kuchokera kudziko limene anatengedwa kukakhala akapolo.+

      Yakobo adzabwerera ndipo adzakhala mosatekeseka komanso mopanda zosokoneza.

      Sipadzakhala wowaopseza.+

  • Yeremiya 44:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Anthu ochepa okha adzathawa lupanga mʼdziko la Iguputo nʼkubwerera kudziko la Yuda.+ Ndipo pa nthawiyo, anthu amene anatsala mu Yuda amene anabwera mʼdziko la Iguputo kuti azikhalamo adzadziwa kuti mawu amene akwaniritsidwa ndi a ndani, mawu anga kapena mawu awo.”’”

  • Ezekieli 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Komabe anthu ena amene adzatsale mʼdzikolo adzathawa nʼkupulumuka ndipo adzatulutsidwamo,+ kuphatikizapo ana aamuna ndi aakazi. Iwo akubwera kwa inu, ndipo mukadzaona njira zawo ndi zochita zawo mudzatonthozedwa ndithu pambuyo pa tsoka limene ndinabweretsa pa Yerusalemu ndiponso pambuyo pa zonse zimene ndinachitira mzindawo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena