Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 4:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Pajatu Yehova Mulungu wanu ndi Mulungu wachifundo.+ Sadzakusiyani kapena kukuwonongani kapenanso kuiwala pangano limene analumbira kwa makolo anu.+

  • 2 Mbiri 36:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nebukadinezara anatenga anthu amene sanaphedwe ndi lupanga+ nʼkupita nawo ku Babulo. Anthuwo anakhala antchito ake+ ndiponso a ana ake mpaka pamene ufumu wa Perisiya unayamba kulamulira.+

  • Ezekieli 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma ndidzachititsa kuti pakhale anthu ena opulumuka, chifukwa ena a inu simudzaphedwa ndi lupanga pakati pa anthu a mitundu ina mukadzabalalikira mʼmayiko osiyanasiyana.+

  • Mika 5:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mbadwa zotsala za Yakobo zidzakhala pakati pa mitundu yambiri ya anthu,

      Ngati mame ochokera kwa Yehova.

      Komanso ngati mvula yowaza imene ikugwa pazomera,

      Yomwe sidalira munthu

      Kapena kuyembekezera ana a anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena