Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Koma ngakhale kuti padzachitika zonsezi, iwo akamadzakhala mʼdziko la adani awo, sindidzawakana mpaka kalekale+ kapena kunyansidwa nawo moti nʼkuwawonongeratu, zomwe zingaphwanye pangano langa+ ndi iwo, chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wawo.

  • Yesaya 27:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa tsiku limenelo nyanga yaikulu ya nkhosa idzalizidwa,+ ndipo anthu amene anali atatsala pangʼono kufa mʼdziko la Asuri+ ndi amene anamwazikana mʼdziko la Iguputo,+ adzabwera kudzagwadira Yehova mʼphiri loyera ku Yerusalemu.+

  • Yeremiya 44:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo anthu otsala a ku Yuda amene apita kukakhala mʼdziko la Iguputo sadzathawa kapena kupulumuka kuti abwerere kudziko la Yuda. Adzafunitsitsa kubwerera kuti akakhale kumeneko koma sadzabwerera kupatulapo anthu ochepa amene adzathawe.’”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena