Nehemiya 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komanso ndinaona kuti Ayuda ena anali atakwatira+ akazi achiasidodi,+ achiamoni ndi achimowabu.+