Deuteronomo 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+ Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
8 Ngakhale ku Horebe, inu munaputa mkwiyo wa Yehova moti Yehova anakukwiyirani kwambiri mpaka kufika pofuna kukufafanizani.+
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+