Ezara 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kodi zoona tiphwanyenso malamulo anu kachiwiri pokwatirana ndi anthu a mitundu ina omwe amachita zonyansawa?+ Kodi tikatero simutikwiyira koopsa nʼkupezeka kuti sipanatsalenso wina wopulumuka?
14 kodi zoona tiphwanyenso malamulo anu kachiwiri pokwatirana ndi anthu a mitundu ina omwe amachita zonyansawa?+ Kodi tikatero simutikwiyira koopsa nʼkupezeka kuti sipanatsalenso wina wopulumuka?