Ezara 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kodi zoona tiphwanyenso malamulo anu kachiwiri ndi kupanga mapangano a ukwati+ ndi anthu a mitundu ina ochita zonyansawa?+ Kodi tikatero simutikwiyira koopsa+ mwakuti sipakhalanso wotsala+ ndi wopulumuka?
14 kodi zoona tiphwanyenso malamulo anu kachiwiri ndi kupanga mapangano a ukwati+ ndi anthu a mitundu ina ochita zonyansawa?+ Kodi tikatero simutikwiyira koopsa+ mwakuti sipakhalanso wotsala+ ndi wopulumuka?