Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 3:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 taona, ndichita mogwirizanadi ndi mawu ako.+ Ndithu ndikupatsa mtima wanzeru ndi womvetsa zinthu+ moti ndi kale lonse sipanakhalepo munthu ngati iwe, ndipo pambuyo pako sipadzakhalanso wina ngati iwe.+

  • 1 Mafumu 10:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru+ kwambiri kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.

  • 2 Mbiri 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chotero Mfumu Solomo inali yolemera kwambiri+ ndiponso yanzeru kwambiri+ kuposa mafumu ena onse a padziko lapansi.

  • Salimo 72:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Ndipo adzakhala ndi anthu omugonjera kuchokera kunyanja kukafika kunyanja,+

      Komanso kuchokera ku Mtsinje*+ kukafika kumalekezero a dziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena