Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ 2 Samueli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli. Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
8 Tsopano mtumiki wanga Davide ukamuuze kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ine ndinakutenga kubusa, kumene unali kusamalira nkhosa+ kuti ukhale mtsogoleri+ wa anthu anga Aisiraeli.
71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+