Salimo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+ Yesaya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mafumu adzakhala okusamalira,+ ndipo ana awo aakazi adzakhala okuyamwitsira ana ako. Iwo adzakugwadira mpaka nkhope zawo pansi+ ndipo adzanyambita fumbi la kumapazi ako.+ Pamenepo, ndithu iweyo udzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndiponso kuti anthu okhulupirira mwa ine sadzachita nane manyazi.”+
10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+
23 Mafumu adzakhala okusamalira,+ ndipo ana awo aakazi adzakhala okuyamwitsira ana ako. Iwo adzakugwadira mpaka nkhope zawo pansi+ ndipo adzanyambita fumbi la kumapazi ako.+ Pamenepo, ndithu iweyo udzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndiponso kuti anthu okhulupirira mwa ine sadzachita nane manyazi.”+