Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi ndine ndinatenga pakati pa anthu onsewa? Ndine kodi ndinawabereka, kuti mundiuze kuti, ‘Uwafukate pachifuwa chako+ mmene mlezi amafukatira mwana woyamwa,’+ pa ulendo wopita nawo kudziko limene munalumbirira makolo awo?+

  • Yesaya 52:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 momwemonso iye adzadabwitsa mitundu yambiri.+ Mafumu adzatseka pakamwa pawo akadzamuona,+ chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo, ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+

  • Yesaya 60:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Alendo adzamanga mipanda yako,+ ndipo mafumu awo adzakutumikira.+ Ine ndinakulanga mu mkwiyo wanga,+ koma chifukwa cha kukoma mtima kwanga ndidzakuchitira chifundo.+

  • Yesaya 60:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena