Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 7:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Atamandike Yehova Mulungu wa makolo athu,+ amene waika maganizo amenewa mumtima+ mwa mfumu, kuti nyumba ya Yehova imene ili ku Yerusalemu ikongoletsedwe.+

  • Nehemiya 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndiyeno ndinauzanso mfumu kuti: “Ngati zili bwino ndi inu mfumu, lolani kuti ndipatsidwe makalata+ okasonyeza kwa abwanamkubwa+ a tsidya lina la Mtsinje,*+ kuti akandilole kudutsa ndi kukafika ku Yuda.

  • Yesaya 49:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Mafumu adzakhala okusamalira,+ ndipo ana awo aakazi adzakhala okuyamwitsira ana ako. Iwo adzakugwadira mpaka nkhope zawo pansi+ ndipo adzanyambita fumbi la kumapazi ako.+ Pamenepo, ndithu iweyo udzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndiponso kuti anthu okhulupirira mwa ine sadzachita nane manyazi.”+

  • Chivumbulutso 21:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Mitundu ya anthu idzayenda mwa kuwala kwake,+ ndipo mafumu a dziko lapansi adzabweretsa ulemerero wawo mumzindawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena