Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova Mulungu wanu adzabweza kwawo anthu a mtundu wanu amene anagwidwa ndi kupita kudziko lina,+ ndipo adzakumverani chifundo+ n’kukusonkhanitsaninso pamodzi kuchokera pakati pa anthu onse kumene Yehova Mulungu wanu anakubalalitsirani.+

  • 1 Mafumu 11:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ndidzachititsa manyazi ana a Davide chifukwa cha zoipa zimene anachita,+ koma osati nthawi zonse.’”+

  • Salimo 30:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+

      Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+

      Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+

  • Yesaya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+

  • Yesaya 54:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena