Salimo 63:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti kukoma mtima kwanu kosatha n’kwabwino kuposa moyo,+Milomo yanga idzakuyamikirani.+