Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Salimo 100:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
5 Pakuti Yehova ndi wabwino.+Kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapo mpaka kalekale,+Ndipo kukhulupirika kwake kudzakhalapo ku mibadwomibadwo.+