Salimo 126:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amene akukhetsa misozi pofesa mbewu,+Adzakolola akufuula mosangalala.+