Yesaya 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+ Yesaya 54:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndi mkwiyo waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+ koma ndidzakuchitira chifundo+ ndiponso ndidzakusonyeza kukoma mtima kosatha mpaka kalekale,” watero Yehova, Wokuwombola.+ 2 Akorinto 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti ngakhale kuti masautso amene tikukumana nawo ndi akanthawi+ ndipo ndi opepuka, masautsowo akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso wamuyaya,+
12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+
8 Ndi mkwiyo waukulu ndinakubisira nkhope yanga kwa kanthawi,+ koma ndidzakuchitira chifundo+ ndiponso ndidzakusonyeza kukoma mtima kosatha mpaka kalekale,” watero Yehova, Wokuwombola.+
17 Pakuti ngakhale kuti masautso amene tikukumana nawo ndi akanthawi+ ndipo ndi opepuka, masautsowo akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso wamuyaya,+